A Malawi akungoyenera kuvala zilimbe pomwe thumba la chimanga la 50Kg lafika pa 100,000 kwacha pa misika ina. Ku madera ena monga Nchalo, Chikwawa ndi Bangula m'boma la Nsanje anthu akugula chimanga 1800 kwacha pa kilo zomwe zikutanthauza kuti thumba la 50 kg ndi (K90,000). Ku Liwonde, Machinga ndi kwa Manase ku Blantyre ka pelo […]
The post Thumba la chimanga lafika pa 100,000 kwacha appeared first on Malawi 24.