Thupi la Mtolankhani odziwika bwino, Martin Chiwanda, aliyika m'manda lero m'mudzi mwa Kalonga, mfumu yaikulu Ntonda m'boma la Mangochi. Pa nthawi ya imfa yake, Chiwanda amagwira ntchito ngati mkulu ofalitsa nkhani ku khonsolo ya boma la Machinga. Malemu Chiwanda anamwalira Lachisanu, pa 2 May, 2025 pa chipatala chachikulu cha boma la Machinga atadwala kwa kanthawi […]
The post Thupi la Martin Chiwanda lalowa m'manda appeared first on Malawi 24.