Mneneri wa chipani cha MCP, Jessie Kabwira, wati ndizotheka kuti zinthu zina zomwe wayankhula mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera Lachisanu potsekulira Nyumba ya Malamulo ndi zonama, koma wati boma lawo lachita chitukuko chomwe sichinachitikeponso m'dziko muno. Izi zili mukilipi yomwe anthu akugawana m’masamba anchezo momwe zikuoneka kuti Kabwira amayankhula ndi anzawo aku chipani cha […]
The post Tikamazimitsa moto sitisankha madzi - Kabwira appeared first on Malawi 24.