Mtsogoleri wakale wa dziko lino yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP), Peter Mutharika wanenetsa kuti masankho amene akubwera pa 16 September ngati patadzachitike m'chitidwe obera, iwo ndi chipani chawo sadzalora ndipo adzathana ndi oyenera kuthana nawowo. A Mutharika ati masankho a m'chaka cha 2020 anavomeleza kulandidwa boma chifukwa sanafune za […]
The post Ulendo uno mukabera zisankho ndidzathana nanu - Mutharika appeared first on Malawi 24.