A Malawi ayembekezere nkhani zakathithi komanso zothyakuka bwino zokhudza zokambirana komanso zomwe zimachita m'nyumba ya malamulo pofuna kuonetsetsa kuti anthu m'dziko muno akutsatira bwino lomwe za momwe zinthu zimayendera m'nyumbayi. Izi zikudza pomwe bungwe la Centre for Social Accountability and Transparency (CSAT) linachititsa maphunziro atolankhani pa 31 May ku Grand Palace Hotel mu mzinda wa […]
The post A Malawi ayembekezere nkhani zakathithi zakunyumba ya malamulo appeared first on Malawi 24.