Mayi Malita Kalirani a dzaka 66 awakwidzinga chifukwa chowaganizira kuti apha amayi awo a Nadimba Kalirani a zaka 82 powaphwanya ndi hamala ku Dowa. M'neneli wa apolisi m'boma la Dowa, a Alice Sitima watsimikiza nkhaniyi ponena kuti zoopsyazi zachitika m'dera la lavu pa 08 December 2024, 10 koloko usiku. Apolisi ati mayiyu ataledzera mowa wake […]
The post Mayi wamangidwa chifukwa chopha mayi ake ndi hamala appeared first on Malawi 24.