Kapena mwina a Malawi tasukutsula mmaso pa njuga mpaka takhaulitsa mzungu? Koma a kampani ya Premier Bet ati vuto ndi chuma. Ndipo tsopano ayamba kutuluka msika wa ku Malawi. Awo paulendo kutsatira DSTV. Kampani yotchuka pa njuga ya Premier Bet yalengeza kuti ikutseka malo onse amene anthu amakakungira ma tikiti a njuga. Malinga ndi chikalata […]
The post Nayonso Premier Bet yazituluka - ati chuma sichikuyenda, ma agent ntchito yatha basi appeared first on Malawi 24.