Apolisi m'boma la Thyolo atsimikiza za imfa ya Ackim Kajiya a zaka 38 omwe adzimangilira ku denga la nyumba yawo kamba ka kusavana ndi mkazi wawo. M'neneri wa apolisi ya Masambanjati m'bomali, Amos Banda wati Kajiya anapezeka atafa kale pozimangilira pakati pa usiku wa lero. Malinga ndi Banda ati malemuwa anali pa mkangango ndi mkazi […]
The post Nkhani za m'banja zatenga moyo wa AcKim Kajiya m'boma la Thyolo appeared first on Malawi 24.