Ngakhale boma limamenyetsa nkhwangwa pamwala kuti m'dziko muno mulibe ufiti, mkulu wina m'boma la Zomba wabwera poyera kutsimikiza kuti ufiti ulipo padziko lapansi pano ndipo wati iyeyo ndi wankulu wa afiti. Mkuluyu yemwe dzina lake ndi John Awufi wa m'mudzi mwa Mbuka dera la mfumu yaikulu Kumtumanji ku Zomba, amayankhula izi mu pologalamu ya 'Tamvani' […]
The post Ufiti ulipo, ine ndimkulu wafiti – watelo bambo wina appeared first on Malawi 24.