M’modzi mwa anthu omwe akhala akutsogolera a Malawi ku ziwonetsero zomwe zakhala zikuchitika mdziko muno posachedwapa, a Bon Kalindo, alengeza kuti ayimitsa kaye ziwonetsero zonse zomwe anakonza kuti zichitike. A Kalindo omwe amadziwika ndi dzina la Winiko, akhala akutsogolera ziwonetsero za 'Malawi salibwino' zomwe amati cholinga chaka kunali kufuna kukakamiza boma la Tonse kuti litsitse […]
The post A Kalindo ayimitsa kaye zionetsero appeared first on Malawi 24.