A Polisi ku Mchinji anjata abambo awiri powaganizira kuti amagulitsa zipangizo za ulimi zomwe anatenga pangongole ku bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) Limited. Malingana ndi bungwe la NEEF, abambowa ndi a Richard Banda komanso Charles Peter omwe ndi mamembala a gulu la Kamwendo Traders ochokera m’mudzi mwa Kamwendo Mfumu yaikulu Zulu m’boma la […]
The post Anjatidwa kamba kogulitsa zipangizo za ulimi appeared first on Malawi 24.