Pomwe chisankho chapatatu chaka cha mawa chino chikununkhira ngati mvula yogwa kutali, chipani chatsopano cha Nzika Coalition chalembetsedwa. Chipanichi Lolemba pa 20 May chinali ku ofesi ya mkulu olembetsa zipani munzinda wa Blantyre komwe chalembetsedwa ndikupatsidwa makalata ochiyeneleza ngati chipani cha ndale tsopano. Poyankhula ndi atolankhani atamaliza kulembetsa chipanichi, mtsogoleri wa chipanichi Christopher Mike Chiomba […]
The post Chipani chatsopano chalembetsedwa ku Malawi appeared first on Malawi 24.