Apolisi mu mzinda wa Blantyre awombera ndikupheratu munthu wina yemwe akuganizilidwa kuti anapita ku polisi ndikukaba mfuti, zipolopolo ndi utsi okhetsa misozi komaso kuvulaza wa polisi wina m’boma la Chiradzulu. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’dziko muno a Peter Kalaya omwe ayankhula ndi nyumba zina zofalitsa nkhani, munthu ophedwayu wazindikilidwa ngati Mike Banda wa […]
The post Apolisi apha oganizilidwa uchigawenga appeared first on Malawi 24.