Apolisi m'boma la Nsanje atsekera matate atatu mchitolokosi atapezeka ndi Nyanga ya Njovu yomwe anatangwanika kutsatsa kufuna kupeza msika. Malinga ndi oyankhulira polisi m'bomali, a Agnese Zalakoma, omwe atsimikiza za nkhaniyi, atatuwa amangidwa nzika zakufuna kwabwino zitawatsina khutu kuti pali njonda zina zomwe zasowa msika wa Nyanga ya Njovu ndipo zikutsatsa katundu oyika anthu m'mavutoyu. […]
The post Awanjata akusakasaka msika wa Nyanga ya Njovu appeared first on Malawi 24.