…Synod ikufufuza abusa ake… Synod ya Nkhoma ya mpingo wa Church of Central Africa Presbyterian (CCAP), yati mwa abusa onse 53 omwe anapita kunyumba ya mtsogoleri wakale Peter Mutharika, m'boma la Mangochi kukachita mapemphero, abusa okwana asanu ndi awiri (7) ndi omwe synod-yi ikuwadziwa. Malinga ndi kalata yomwe Nkhoma Synod yatulutsa yomwe watsimikiza mlembi wa […]
The post CCAP Nkhoma Synod yakana mapemphero omwe anachitika kwa a Mutharika appeared first on Malawi 24.