Kuno zipatalazo kulibe, kuno manyumbawo kulibe, kuno ma Mega farm wo kulibe, bodza la Chakwera kuwonekera poyera zamanyazi Ma khonsolo osiyanasiyana akupitilira kumukana Chakwera monga muja Petro anamukanira Yesu. Makhonsolowa akukanitsita kwa mtu wagalu kuti zina zomwe anakamba Chakwera mu SONA yake lachisanu lapitali ku nyumba ya malamulo ndi bodza lamkukhuniza. Khonsolo ya Boma la […]
The post Chakwera akukanidwa kulikonse appeared first on Malawi 24.