Phungu wa dera la pakati m'boma la Mangochi, Victoria Kingstone, watsutsa kwa ntu wa galu zomwe wanena mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera, kuti boma lamanga chipatala cha Namiyasi. A Chakwera anafotokozera Nyumba ya Malamulo Lachisanu kuti pansi pa ulamuliro wawo amanga zipatala zing'onozing'ono 25 m'boma la Mangochi zomwe ndi kuphatikizapo chipatala cha Namiyasi. Komabe, […]
The post Kulibe chipatala cha Namiyasi ku Mangochi - Kingstone appeared first on Malawi 24.