Milandu iwiri ya katswiri ochita zisudzo Tumpe Mtaya yemwe amadziwika ndi dzina loti 'Phwedo' inalowanso m'bwalo la milandu la Lilongwe Principal Resident Magistrate kuti katswiriyu apitilire kuyankhapo. Phwedo lero Wakana pamaso pa bwalo milandu yake yonse iwiri; ogonana ndi mwana osakwana zaka 18 komanso mlandu wina ozembetsa mwana, yomwe a mbali ya boma anamumanga nayo. […]
The post Milandu ya Phwedo inalowanso m'bwalo lero, oweluza wayimitsa kaye appeared first on Malawi 24.