Mayi wakale wa fuko la Malawi a Gertrude Mutharika alangiza anthu m'dziko muno makamaka amai kuti pamene nyengo yokopa anthu mu chisankho cha chaka chino ikuyandikira, asakopeke ndi andale adyera amene amakhala kalikiliki kugawa katundu osiyanasiyana ndi cholinga choti azavoteledwe m'mipando yosiyanasiyana. A Mutharika ayankhula izi Loweruka m'boma la Balaka kumene anali mlendo olemekezeka pa […]
The post Musakopeke ndi andale adyera—Mayi Mutharika alangiza amai appeared first on Malawi 24.