Katswiri pa ndale George Phiri wati aphungu a Nyumba ya Malamulo ena, asatangwanike ndi kuwasangalatsa anthu akwawo ndi zinthu lero pomwe mu zaka zisanu zonse zomwe zapitazi akhala akudya okha, pomwe atsindika kuti anthu akwawowo pano anazindikira kuti 'inuyo si munthu oyenera.' A Phiri ati pa zaka zonse aphungu ena kufikira lero alibe choti akhonza […]
The post M'zaka zisanu zonsezi amene mwadya ndinuyo aphungu, anthu akwanu musawasangalatse lero lokha - George Phiri appeared first on Malawi 24.