Lero m'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wavwavwaniza a Malawi ndi bodza lankunkhuniza ponena kuti boma lake lachita zitukuko za nkhani nkhani m'dziko muno zomwe ambiri akupukusa mutu opanda nyanga. Chimodzi mwa zitukuko zomwe Chakwera anati boma lake lachita ndi kumanga nyumba za a polisi zokwana 24 m'boma la Likoma. Koma Malawi24 yapeza kuti m'bomali […]
The post Walifwanthamula bodza: Chakwera anamiza a Malawi pa zitukuko appeared first on Malawi 24.