Zadziwika kuti m'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera lero wanamiza a Malawi ku nyumba ya malamulo pomwe anati Boma lake la kongelesi lamanga nyumba 29 za a Polisi mu m'boma la Phalombe. Koma khonsolo ya bomali yakana kwa mtu wagalu kuti zomwe wakamba Chakwera ndi zabodza zedi, chifukwa mu bomalo mulibe ngakhale nyumba imodzi ya […]
The post Zamanyazi: Chakwera wanamiza mtundu wa Malawi, ku Phalombe sikunamangidwe nyumba 29 za Polisi appeared first on Malawi 24.