Timu ya mu ligi yayiku mdziko muno ya Premierbet Dedza Dynamos yadyelera maso ntchito za mphunzitsi wakale wa Mighty Wanderers Alex Ngwira, kulowa m'malo mwa a Andrew Bunya omwe awachotsa ntchito ku timuyi masiku apitawo. Wachiwiri kwa wapampando ku timu ya Dedza Mavuto Mugode atsimikiza za kufika kwa a Ngwira ku timu ya Dedza ponena […]
The post Dedza Dynamos yazomola mphunzitsi wakale wa Wanderers Alex Ngwira appeared first on Malawi 24.