Nduna ya Zachuma, a Simplex Chithyola Banda ati boma lachotsa msonkho wa 16.5% Value Added Tax (VAT) pa buledi (bread) ndi ma sikono (buns) ndipo akuyembekezera kuti mitengo ya Bread ndi mabanzi zitsika. Izi zadziwika pamene ndunayi imapeleka ndondomeko ya zachuma yokwana 8.05 trillion Kwacha ya mchaka cha 2025/2026, kuchoka pa 6 trillion Kwacha ya […]
The post Masikono atsike mtengo - Chithyola appeared first on Malawi 24.