Zadziwika kuti woyimba Patience Namadingo yemwe pakatipa watchuka ndi nkhani yoti amatchaja K10 million kukaimba malo amodzi, Lachinayi sanatenge nawo K200,000 yomwe nyumba ya chifumu idapeleka kwa achinyamata omwe anakacheza ndi m'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera munzinda wa Blantyre. Paja khoswe wapatsindwi adaulura wapadzala! Izi waulura ndi Refilwe Ntopa, m'modzi mwa omwe anali nawo […]
The post Namadingo sanapochere nawo K200,000 ku nyumba yachifumu ya Sanjika appeared first on Malawi 24.