Chuluke chuluke ndi wa njuchi koma umanena yomwe yakuluma, a Malawi ochuluka awonetsa kugwa mchikondi ndi nyimbo yomwe yatenga kale malo ’Pano' ya Shaffie Phiri yemwe amadziwikaso kuti Driemo. Munyimboyi yomwe ndiyachikondi ndipo yatulutsidwa la chitatu sabata ino, munthu osweka mtima akudandaula kaamba ka kutha kwa ubwezi ndi okondedwa wake. Odandaulayo akufusa bwezi lake lomwe […]
The post ’Pano' ndi Driemo appeared first on Malawi24.