Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi ati nthawi zina zimadabwitsa kuti atsogoleli ena a mipingo amakhala ngati ntchito yomwe ilipo ndi yongodzudzula andale kuposa kuwathandiza anthu kukalowa kumwamba. Poyankhula pa mwambo wa maliro a Chikumbutso Mtumodzi ku Chankhungu m'boma la Dowa lero, a Usi ati ndale zili potelopo, koma atsogoleri a mipingo […]
The post Usi wadandaulira mipingo kuti isamangodzudzula andale kuyiwala kuthandiza anthu kukalowa kumwamba appeared first on Malawi 24.