Mkumano wa mtsogoleri wa dziko la America a Donald Trump ndi mtsogoleri wa dziko la Ukraine a Volodymyr Zelenskyy wathera panjira pomwe akulu akulu awiriwa athilana mawu. Mkumanowu unakonzedwa ndi cholinga choti mayiko awiriwa akakambilane za momwe angaimitsire mtsogoleri wa dziko la Russia a Vladimir Putin kuthira nkhondo dziko la Ukraine. Ngati mbali imodzi yoti […]
The post Zathera panjira: Zelenskyy wachoka pa mkumano ndi Trump atasemphana chizungu appeared first on Malawi 24.