Timu ya dziko lino ya mpira wamiyendo ya 'The Flames' yafika mu mzinda wa Pretoria m'dziko la South Africa kukonzekera kubwerezana ndi timu ya dzikolo ya Bafana Bafana Lamulungu lino mu masewelo a mu mpikisano wa CHAN. Flames yanyamuka lero ku m'mawaku kudzera pa bwalo la ndege la Kamuzu mu mzinda wa Lilongwe ndi osewera […]
The post Flames yafika ku South Africa kukonzekera chibweleza appeared first on Malawi 24.