Zina ukamva kamba anga mwala! Lachitatu kudali chiphwete chosakanikirana ndi chisoni pa msika wa Sumbi ku Monkey Bay m'boma la Mangochi pomwe mkulu wina amakodza usipa chifukwa choswa mtedza ndi mkazi wa mwini. Malingana ndi wailesi ya Dzimwe, pa 28 March, 2025, njondayi itamva kutentha mthupi, idakakhuthulira ukali wake wonse pa mayi wina ku Makanjira […]
The post Mshomoli akodza usipa appeared first on Malawi 24.